Pali ma phone Ena akumatengedwa pa ngongole ku shop mafoniwa ndi techno spark 7, spark 8c,pop 5 komaso camon 18 mafoniwa akumalipilidwa pa ngongole pa week kapena pa mwezi mpakana Chaka chithe ukapanda kulipira monga mwamgwilizano mafoniwa eni ake akumawalocka zomwe zikumafunika kuti alipilidwe Kaye kuti awapange unlock mafoniwa Ali mu mdzina la… See more
$5