Cages

Mwina mwakhala mukuchita ulimi wanu wa mbalame koma mumasakasaka makola amakono ngati awa, yankho mwalileza kuno ku humble steel furniture and fabrication tepezen pa selipa kuti mupezekoso anu pa number iy 0995379006 /0882209830 pomwe tikupezekela mu lilongwe kawale 2 pafupi ndi corner ya barracks opposite chipatala cha umunthu medical clinic ndipo mitengo yake ili motele khola la nkhunda 110,000mk, khola la akalulu, 220,000mk, khola la nzinzili likuyambila 240,000mk, lankhuku za nyama 250,000mk, ndi nkhuku za mazila 270,000mk.

$240

seller's name'
Name: Oscar K
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 21 November, 2021

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0995379006
seller phone number Phone Number: 0882209830

Product Images

product image 0
Image 1 of 4
product image 1
Image 2 of 4
product image 2
Image 3 of 4
product image 3
Image 4 of 4
Loading recommendations...