Makolo amulilongwe mwanatu amafunika chisamaliro chabwino nthawi zonse ..makamaka akamapita ku school ..bus iyi tipatseni zochita anawo asamalidwe tizikawasiya mosamalitsa... Mtengo wadzuwa tikambilana 0995379882
$12