Sausage Training Training MZ LL BT KA

Ndinu a business? Mumangokhala kapena muli ndi mbale amene akungokhala koma mukafunitsitsa atapeza zochita ? ,ife a House of Solutions timaphunzitsa kapangidwe ka sausage M'madera osiyana siyana Malawi muno* Munthawiyi onse amene mukufuna kupanga Sausage komanso ma meat balls mwai uja wafikanso ku Training timaphunzitsa izi�� 1. Entrepreneurship skills 2. *How to make Sausages three types* i. Lollie Beef Sausage ii. BBQ Beef Sausage iii. Commercial Beef Sausage. 3.How to make meatballs Training imeneyi muzangobwera chilichonse muxachipeza konko ,komanso Kumaliza Training imeneyi muzalandira machine opangira sausage a ulele (Manual) ,,,,Training fee ndi *Mk12,000.* kumaliza training aliyense azatenga sausage imene mwapanga popita kunyumba komanso ma spice oyambira after Training Mwa ulele��������� Ndalama muzapereka ku Training konko ,pobwera muzangotenga Jumbo yoikamo sausage yanu popita kunyumba basi... *Lilongwe Sausage Training on 3rd July 2021* Malo ndi Livimbo primary school. *Blantyre Sausage Training on 3rd July 2021* malo ndi Limbe primary school. *Mzuzu on 31st July 2021 Malo St Andrews primary school. For details drop your number, or call/text on WhatsApp on this line...0999555589. Or join the link below��� https://chat.whatsapp.com/DG7U8ehzjEcEAGupFXQlqc

US$12,000

seller's name'
Name:
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 01 July, 2021

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0999555589

Product Images

product image 0
Image 1 of 4
product image 1
Image 2 of 4
product image 2
Image 3 of 4
product image 3
Image 4 of 4
Loading recommendations...