👩🦰 #GOLDIE "Panopa music ya ku Malawi ikulowa pansi kamba konena kuti tili ndi anthu ozipereka ochepa omwe amafuna kubweretsa poyera maluso a Achinyamata ochulukirapo amene ma access to exposing themselves alibe. Zimangoona kuvuta koma anthu a Talent nde alipo Mbweeeee!!, Komabe ngakhale zili Choncho, the little we have tiyeni tiyembekezere zopambana zochuluka zochokera mmaluso amenewa ndipo pano tikunenetsa… More