Ma plot onseo pamodzi mtengo ndi 4 million contract 0990455680
Price: FREE
Private Seller: Joe-Joshua B
Madzi alipo koma magetsi ayi but Ali pafupi price 5.8 million with discount 0990455680
Price: FREE
Private Seller: Joe-Joshua B
Plot for sale old airwing 60m by 60m,with valid papers,water & electricity close. Plot within development area. 100m from the road. Going for 7million. For more details inbox me/call 0993046604
Price: FREE
Private Seller: Max M
Madzi ndi magetsi zili pafupi kwambiri Malowa ali pabwino kwambiri Phone number yanga ndi 0992335517/0885837201
Price: FREE
Private Seller: Mwendothamanga P
Kupeleka pang'ono pang'ono nzotheka 0990455680
Price: FREE
Private Seller: Joe-Joshua B
5 FARMS for sale (both 5 hectares which means 10 acres Each ) Location : kapiri, MCHINJI Contact : 0997790007
Price: $650,000
Private Seller: Success B
Tilindimaplot abale anzanga abwino2 plot size 15/30 ntengo: mk 550.000 pangongolenso zikutheka myezi ingapo Zadongosolo miseu yachenso osat zachinnabalala Cll 0992710149 Cll 0888704445
Price: $537
Private Seller: Mathelo S
RESIDENTIAL PLOT FOR SALE IN NYAMBADWE WELL POSITIONED ALREADY BRICK FENCED NEAR NYAMBADWE HOSPITAL GOOD PLOT PLOT SIZE 51M BY 46M BY 19M DEED AVAILABLE ASKING PRICE K38MILLION CALL 0999915599/0888825740
Price: $38,000,000
Private Seller: Semu J
Plot yaikulu. Kuli main house komanso nyumba zina za rent komanso mashop awiri olumikizana ndi mpanda kutsogolo. Ku mpanda komanso nyumba zonse zamagesi. Ndalama zonse za rent zomwe zimatoleledwa pamwezi ndi 135,000 kupatula nyumba yaikulu yomwe amakhala enuwake koma kupangitsa rent itha kukhala 70 to 80 thousands. Mtengo omwe tikufunapo ndi 7.5 million. Lilongwe 0999809730/0884552255.
Price: FREE
Private Seller: Samson K
Ofuna plot or the whole area your choice Wap/call 0882 14 52 94
Price: MK7
Private Seller: Chiku K
And 2.7 both kupeleka pang'ono pang'ono nzotheka 0990455680
Price: FREE
Private Seller: Joe-Joshua B
Madzi ndi magetsi Ali pafupi komanso mseu Mtengo ndi 4.5 million Phone number yanga ndi iyi :0992335517/0885837201
Price: FREE
Private Seller: Mwendothamanga P
Nyumbayi ili ndi three bedroom, sitting room, dining room, kitchen, stores, two bathroom, two toilet Size yanyumba ndi 8 by 30 meters Mtengo ndi wokambirana Nyumbayi ili pafupi ndi praise private school Ngati mwayikonda nyumbayi kuti mukamalizitsa nonkha tiyeni tikambirane pondiyimbira phone number yanga ndi:0992335517/0885837201
Price: FREE
Private Seller: Mwendothamanga P
We have Farms for Sale in Chikwawa, Zomba, Machinga, Balaka, Salima, Nkhotakota, Nkhatabay Mnchinji and Kasungu. Inbox us for enquiries. +265998253443
Price: $240,000,000
Private Seller: Kapira N
Malowa alipafupi ndi mseu wa tala ndi 150 meters yokha mwafika pa plot Madzi ndi magetsi alipafupi Phone number yanga ndi:0992335517/0885837201
Price: FREE
Private Seller: Mwendothamanga P
I have two Plots for Filling Station, one is in Lilongwe Chimwanza Trading one acre and another one is in Mangochi Monkey-bay road opposite Goshen City two acre 18million and 25million respectively for more information Contact us on 0995677348/0888966222 Whatsapp 0995677348
Price: MK20
Private Seller: Petros C
FARMLAND FOR SALE IN MANGOCHI Mk 750MILLION NEGOTIABLE
Price: MK750
Private Seller: Prince S
Plot for sale in City Centre. 0.2 hectares. Title deed available. Mk250,000,000. Call: 0998253443
Price: $250,000,000
Private Seller: Gwiyule M
Malawi wayaka moto imbani kapena Whatsapp pa 0888384334 ngati mukufuna kuthandizidwa za visa ya USA South Africa Germany UK Netherlands UAE China . NOTE: Ine si Embassy ndipo sindipeleka Visa ndine, ndimangothandizila chabe kuti mupeze Visa yo
Price: R888,384,334
Private Seller: Hugh M
MULANJE MUDZI MWA KUKADA PAFUPI NDI SCHOOL YA MTHULUWE SEU WAKU PHALOMBE HOLY FAMILY HOSPITAL "PHEPETE MWA MTALA "45 BY 35 METRES @ 3.650 MILLION "MADZ NDI MAGETS PAFUPI "GALIMOTO IKUFIKAPO WHATSAPP +265888313869/+265998976464
Price: $1
Private Seller: Markreens K
MACHINJIRI AREA 11 FEDALATION "27 BY 16 METERS @2.5 MIL NEGO- "ALREADY IN BRICKED FENCE "POFIKA GALIMOTO MADZ NDI MAGETS PAFUPI KWAMBIRI +265888313869/+265998976464
Price: $1
Private Seller: Markreens K
K7.2 million Watsapp 0888177344
Price: MK7,000,000
Private Seller: Wesly K
HOUSE FOR SALE IN NEWLANDS WITH THE FOLLOWING ATTRIBUTES 4BEDROOMS SWIMMING POOL ASKING PRICE K250MILLION CALL 0999915599/0888825740
Price: $250,000,000
Private Seller: Semu J
Plot for sale at Airwing (Real Airwing not Baron) 50m x 40m, going at K9.5 million. Contact: 0999061449 /0888115015
Price: MK9,500,000
Private Seller: Dumisani S
TIMAPEZEKA NDI NYUMBA ZOGULITSA, ZA RENT, KOMANSO MA FARM, TIMBILENI PA 0998950006 / 0880026077.
Price: FREE
Private Seller: Samson L
Completely fenced plot with gate in area 49, Newshire. Not far from Gulliver stage. Its 15 by 30. Water already connected on the plot with servant quarters. City papers available. For prices and and other decent plots, visit www.atsogo.mw/properties, email property@atsogo.mw, call/WhatsAp +265 888 05 23 62 . Facebook@Atsogo Estate Agent, Twitter@AtsogoAgent. Office is in area 47/4
Price: MK1
Private Seller: Atsogo M
15 by 30 ikugulitsidwa PLOT pa mtengo wa 1 million kwacha kukambirana kulipo museum yabwino imbani kapena wap pa 0996103044 muzathanidizidwa moyenera
Price: $1
Private Seller: Edwin J
COMMERCIAL PLOT FOR SALE IN CHITAWIRA ALREADY BRICK FENCED DIMENSIONS 0.371HACTRES ASKING PRICE K80MILLION CALL 0999915599/0888825740
Price: $80,000,000
Private Seller: Semu J
Decent plot for sale in Likuni, just opposite CICCOD houses. Water and electricity available. Ita 953 square meters. For 3 town town houses. For prices please visit the website www.atsogo.mw/properties Call/WhatsApp +265 888 05 23 62 Email property@atsogo.mw Office: 47/4
Price: MK1
Private Seller: Atsogo M
PLOT FOR SALE ALONG CHILEKA ROAD TEN MILES VERY FLAT ASKING PRICE K1.5MILLION CALL 0999915599/0888825740
Price: $1,500,000
Private Seller: Semu J
BEACH PLOT FOR SALE IN SALIMA
Price: MK38
Private Seller: Prince S
Farm for sale in nkhotakota namakwata village Mk 50million negotiable
Price: MK50
Private Seller: Prince S
Buy land from us at 6miles just after police roadblock at an affordable price For more info contact: 0999451731
Price: $1
Private Seller: Brave N
Malo ogulitsa kulilongwe Area23 malo otsika Mtengo abwino Pali nyumba imodzi yaikulu bwino iinuu!! M
Price: FREE
Private Seller: Charity K
Farm for sale in Kasungu Kawamba area. 10.8 hectares 12.5 million 0880378967
Price: $1
Private Seller: Amanda M
TIKUCHITITSA RENT MINDA KOMANSO WOFUNA KUGULA NDIZOTHEKA KU BALAKA MADERA AWA:
Price: $1,000
Private Seller: Jonathan K
Plot for sale Bwemba vertenary, plot size 15x30 miters, Partly fanced, price mk 5 million negotiable. Contact number: 0999603341/0996190999 WhatsApp.
Price: $5,000,000
Private Seller: Phatso L
Plot for sale area 25/4, plot size 15x30 miters, water and electricity averable, already developed area. Price mk 2.8 million negotiable. Contact number: 0999603341/0996190999 WhatsApp.
Price: $2,800,000
Private Seller: Phatso L
PLOT YOGULITSA IYI KU AREA 51 MADZI,MAGETSI ZILI PAFUPI, PALI FOUNDATION PA PLOT PA, MSEU MPAKA PA PLOT, MPHEPETE MWA NSEU WOPITA KWA NTABA. PRICE 5.5 MILLION, SIZE 55m BY 40m. Call me on. 0889985807
Price: FREE
Private Seller: Gray N
Plot for Sale in Zomba Near Chanco Approximately 60m by 50m Ideal for Hostels Price Negotiable Call/Whatsapp +265 99 571 9443/ 0999928497/
Price: MK9
Private Seller: James C
Chonde chonde musakalambile pa rent kapena kubwelela kumuzi malo tilinao Town muno ochipisitsa. Tioezen muzaone ku Chileka tili ndimalo ochipisitsa nthawi isanathe. Plot 350.000 kmanso 500.000 Kmanso mutha kupeleka kwa myezi itatu! Bwanj pamenepo? Taimbani pa: 0992710149 / 0888704445 Asakunamizen kut mubeledwa zaoneni kae
Price: $487
Private Seller: Mathelo S
Malo adakalipo kuno ku Chilaweni kudutsira pa MBC or pa Ken Blows kulowera ku mmawa ndipo ndiabwino kaya mufuna kumangapo nyumba ngakhale kulimapo owafuna andiyakhule pama numbers awa +265888077578 or +265982523402
Price: FREE
Private Seller: Nelson R
Plot for sale at Airwing. Developed Area Size 15 by 30 at K1.3m 0882197073
Price: FREE
Private Seller: Emmanuel M