Am selling open view Decorder almost new remote control Included call or WhatsApp 0780796331
Price: R450
Private Seller: Johnn Y
Zagulen kilile kiliye decoder Almost new 15k remote iliposo
Price: $15
Private Seller: Shadreck F
Am selling brand new startimes Decorder projectors. Price MK300 000. Location-Mzimba boma. Contacts 0994673927 or 0884609425 both are on WhatsApp
Price: MK300
Private Seller: Winter C
For dish installation and tv wall mounting please call/WhatsApp 0999744182 lilongwe and surrounding area's.
Price: FREE
Private Seller: Chimwemwe K
DSTV Explora registered in RSA muntha kumalipira komwekuno zotheka ndi standard bank Am in zomba model 3a With hard drive 1000GB Seagate (1tb) Video 2.5 HHD MK50,000
Price: $50,000
Private Seller: Pencil G
No monthly fees its free to air (Yaulere tosalipila pa mwedzi) Watsapp or calls on 0880578371
Price: MK95,000
Private Seller: Fredrick P
Zagureni ma decoder awa pa mtengo otsika asanakwere tili mu Limbe Sports kathithi Imbani 0996278482 kuti zisakuphonyeni
Price: MK65,000
Private Seller: Amuna J
Buy StarSat Extreme 9990H decoder with more than 1000 channels available.
Price: MK78,000
Private Seller: Emmanuel A
Ma guy's tatengani ma decoder awa ya malawi ndi South Africa Almost new yamalawi 10pin ya jonz 25pin .....0882373978
Price: $25
Private Seller: Mphatso O
Zatengeni gotv ya new iyi @30pin only 0999626854
Price: $30
Private Seller: Gift I
Mwaswela bwanji amalawi amzanga kumene muli ndangofuna kukudziwitsani kuti Ngati mukufuna kupeza chithandizo mwachangu kunkhani yachuma ndi Zina zambiri popanda Ku kwimila muyimbileni gogo uyu akuthandizani nditu akuthandizani pamvuto lililotse limene muli nalo ineyo ndimwa mmozi amene ndathandizidwa I know kuti enanu muzinyozela komano ndikudziwa See more
Price: $1
Private Seller: Dct K
If ur Interested Pls call on 0997216188 0885156540 Blantyre
Price: MK90
Private Seller: Davie M
MONI!! ABALE ANZANGA CHAKA CHINO CHA 2023 pamene ena akusangalala ena ndi pamene akulira chifukwa chonamizidwa. Nsing'anga weni weni mungaziwe bwanji amalawi? ndili pano kukuziwitsani kuti fikani kwa ine pa More
Price: FREE
Private Seller: Thee A
Fairly used open view decoder iyi Zatengeni muzione ma channels aulere Ndili zomba songani Price: 50k 0999773323
Price: $50
Private Seller: Bambo J
Katundu wabwino uyu wabwino uyu wachangu ndan angonyamula zonse pantengo okambilana 0993187920/ 0882490143
Price: FREE
Private Seller: Canastar N
Halla me on 0992060140
Price: FREE
Private Seller: Wilfried C
Very good suit new sinavalidwepo Tinagula pa shein koma ikukula
Price: MK70
Private Seller: Kachingwe N
Amene ali ndi Zuku Decoder wamkulu uja (woyambirira komanso wokhala ndi free to air channels) tiyankhulane chifukwa akufunika kwambiri. Komanso amene ali ndi ma gas battery okutha koma akuluakuku tikambirane mtengo.
Price: FREE
Private Seller: Msekanawana C
SA registered Dstv Decoder for sale in box for price
Price: FREE
Private Seller: Nick S
DSTV Explora utra Decoder going at a giveaway price of 10,000 kwacha
Price: FREE
Private Seller: Farook A
Tabwela wachanguyo adzatenge gotv decode and charger pa mtengo ongovana need fast cash serious buyer inbox 0994157738
Price: FREE
Private Seller: Seer O
Omwe ali ndi second hand open view decoder kapena laptop tisinthane ndi bland new Star sat decoder. WhatsApp only pa 0996033100.
Price: FREE
Private Seller: Jack B
Open view decoder for sale new sealed 70k contact me on wap 0882736315 or call 0993612595
Price: FREE
Private Seller: Ramzy Z
Bland new Star sat decoder swap with second hand open view decoder , if interested whatsapp on 0996033100.
Price: FREE
Private Seller: Jack B
Chilochonse chilipo....only serious business....0885869956....
Price: MK25
Private Seller: Båby H
Pls call for Fast Business 0997216188 0885156540 Blantyre and Surrounding Areas
Price: MK8
Private Seller: Davie M
Tiguliseni DSTV decoder mu Lilongwe 0993928082 cash iyi
Price: $18
Private Seller: Nersto E
Plazma for sale good condition ndika Govt kake pomwepo ndikupezekela ku 23 pa tank.. tiyimbileni pa number izi pompano musachedwe 0995016330/0881844768
Price: $90,000
Private Seller: MJ T
Pls call for Fast Business 0997216188 0885156540 Blantyre I deliver/Send anywhere withn Malawi
Price: MK4,000
Private Seller: Davie M
Sankhanipo apa mabwana katundu uyuuu wabwino
Price: FREE
Private Seller: Brian H
Nyumba yogulitsa ku Blantyre kulunzu,mbairi mwa msewu, malowa ali pabwino ok, 1 Pali nyumba 4 za rend, 2 madzi Alipo, 3 magesi alipo, 4 msewu ulipo, 5 kumpanda komanso ku space yaikuru mutha kikako nyumba ziwiri, 6 pari ma barber shop atatu ndi shop, Pamwezi timatolara 266 thousand kwacha. Mtengo woyambila ndi 45 million kwacha, kukambilanananso kulipo. Numbers 0999111635 call or Whatsapp, 0888651347 call only. Malo ake ndi awa
Price: FREE
Private Seller: Josephy B
MAWA TAZATENGENI DECODER YA DSTV PAMTENGO ONGOTOLA 18pin basi kumvanaso kulipo call 0991800053
Price: $18
Private Seller: Qhabanga G
Huawei nova y90 for sale, and openview decoder, I'm in Lilongwe mbwatalika, whatsapp 27711279174
Price: R350,000
Private Seller: Pentagon B
Guys ndimafuna decoder ya kiliye kiliye Yolowa HDMI and USB Ikhaleso ndi remote control
Price: FREE
Private Seller: Justice N
Pali GoTv latest version Hdmi,usb,av slots 10 meter cable Aerial Remote with batteries 1 month old Blantyre
Price: FREE
Private Seller: Joseph Y