I'm looking for bicycles kabaza type to buy within mzuzu zikhale or 5 zikhale mu good condition ndipezeni osaopa. Mitengo should be flexible
Price: FREE
Private Seller: Doctors M
Preloved original za uk Hoover 200pin bicycle 170pin lilongwe kulikonse timatumiza wap 0992685566
Price: $200
Private Seller: Lucky M
Bicycle for sale,good condition .Almost new.3months old.0998882407 call/WhatsApp.
Price: MK130
Private Seller: Mwawi N
Brand New Mkango Bicycle for sale
Price: $120
Private Seller: MALAWI B
MFUTI KU MFUTI.. Mwala Ku mwala katundu wabwino ...tipezeni pa 0882381643 ...muziyenda mutakhala ma bwana.....mbiteeee ....wanu wanu ine akatundu business yopanda madando
Price: MK1,200,000
Private Seller: MALAWI T
Sports bicycle muzipitira kunsika kogura masamba aka
Price: $65,000
Private Seller: FREE M
Tipezesen Bicycle yabho titenge mountain bike ya medium inbox timvane Ndili Blantyre
Price: $1
Private Seller: blantyre c
Katundu apite moyo usale Computer set ndipatseni 145 need serious buyers njingayo ndipatseni 140 fan ndipatseni 25pin location Bvumbwe close to chigumula market Whatsapp or call if interested 0992666008
Price: FREE
Private Seller: HOUSES A
Katundu opanda minyama uyu dzatengeni mu chinsapo 1 (0997702554
Price: MK285,000
Private Seller: Aggrey M
Buffalo bicycle for sale Mk 190 000 0888282726
Price: MK190
Private Seller: James F
Njinga yabwino za mpikisano zija 0994549541 Ekwendeni
Price: MK110
Private Seller: Goffat D
Running out of stock Get yours today 0993699616 / 0997464767 Free Delivery around Mzuzu CTS/ Smart Delivery/ Speed
Price: $300,000
Private Seller: Anthony K
Njinga ya kabaza iyi zatengen kukambilana kulipo
Price: MK95,000
Private Seller: Kwathu P
Selling this bike with engine at 170K negotiable
Price: MK170,000
Private Seller: MALAWI -
Am selling mountain bicycle everything is good for more information WhatsApp 0881686323
Price: $1,800,000 Now $180,000
Private Seller: CARS A
Red and black Almost new Strong and original metalics Price negotiable 0888747950 calls and WhatsApp
Price: MK8
Private Seller: MALAWI T
Pezani yanu if u interested call or wap 0990429366/0881243936
Price: $180,000
Private Seller: LILONGWE C
Ndikugulitsa njinga yabwino no problems. Kungotenga ndikukwera ulendo wapsa. Tikufunako k150,000 yokha. Tiyimbireni pa 0897281900 Or whatsap +27848701869
Price: MK150
Private Seller: Hajji F
Wabwera katundu uja ndameneyu pamtengo ongo Taya basi. xmas asandiduse 95pin basi
Price: FREE
Private Seller: Hot S
Timagula makatundu onse amene simugwilitsa ntchito,kaya owonongeka kapena amagwilabe ntchito bwinobwino,zisakutheleni malo Mnyumba, mu stores,warehouse tigulitseni Mitengo yokambilana,katunduyi ndi monga Cookers,mincooker, microwaves,TVs,radios,home theatres,speakers,sofa sets dining sets,computer sets,laptops,children bicycles,deepfryers,ricecookers,sandwich makers,chappat makers,fan,irons,extensions,hotplates ,refrigerators, coffeetables, entertainment units,kettles etc Call or watsapp 0888451541/0991938407
Price: FREE
Private Seller: Freddie Y
Bweretsani zomwe zilipozo muzatenge njinga yangati iyi ya new one mukaiyamba nokha iliso mkatoni Area 23 ku tank
Price: FREE
Private Seller: Arther P
SPORTS BICYCLE ALMOST NEW 5 MONTHS COME AND BUY ONLY 87 THOUSAND KWACHA LILONGWE AREA 13 CITY CENTER CALL ON 0987747023 TIVANE
Price: $87
Private Seller: Paul M
Mundipatsa zingati Ndili ndi njinga ngati iyi koma yangayo ili mkatoni (carton) brand new mukamangilira nokha chili chose chilipo kale Area 23 ku tank Wa serious make your offer ku inbox
Price: FREE
Private Seller: Victoria S
Mundipatsa zingati Ndili ndi njinga ngati iyi koma yangayo ili mkatoni (carton) brand new mukamangilira nokha chili chose chilipo kale Area 23 ku tank Wa serious make your offer ku inbox only
Price: FREE
Private Seller: Clement P
Lifo motorbike..fully functioning..I need fast cash ..ndiomboleni fast fast and I need MK600,000...
Price: MK612,000
Private Seller: Gideon D
Lets enjoy the life with beautiful things. Ka UK scutta aka zapa uk pa boma. With no mistake almost new. Kosavutaso kunyamula kungopinda pinda basi.
Price: MK75
Private Seller: MALAWI S
Gud bike just buy and ride ndiyankhuren poimba 0986599343 timvane
Price: MK180
Private Seller: Msungwe L
Katundu wabwino kukwera kumapita With tubeless tires
Price: MK70,000
Private Seller: winners c
Humber ndi Roma ,zakapalsa zabwino zili ndi Dan break ndikuodetsa komaso imodzi imodzi.
Price: MK150
Private Seller: Lukman P